Yeremiya 18:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma iwo anati: “Zimenezo ayi!+ Ife titsatira maganizo athu, ndipo aliyense wa ife adzachita zinthu mouma khosi, mogwirizana ndi mtima wake woipa.”+
12 Koma iwo anati: “Zimenezo ayi!+ Ife titsatira maganizo athu, ndipo aliyense wa ife adzachita zinthu mouma khosi, mogwirizana ndi mtima wake woipa.”+