Yeremiya 18:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma anthu anga andiiwala.+ Chifukwa akupereka nsembe* kwa chinthu chopanda pake+Ndipo akuchititsa kuti anthu amene akuyenda mʼnjira zawo, mʼnjira zakale, apunthwe,+Akuwachititsa kuti ayende mʼnjira zolakwika zomwe ndi zokumbikakumbika.*
15 Koma anthu anga andiiwala.+ Chifukwa akupereka nsembe* kwa chinthu chopanda pake+Ndipo akuchititsa kuti anthu amene akuyenda mʼnjira zawo, mʼnjira zakale, apunthwe,+Akuwachititsa kuti ayende mʼnjira zolakwika zomwe ndi zokumbikakumbika.*