Yeremiya 18:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho dziko lawo lidzakhala chinthu chochititsa mantha+Komanso chimene anthu azidzachiimbira mluzu mpaka kalekale.+ Aliyense wodutsa pafupi ndi dzikoli adzaliyangʼanitsitsa mwamantha ndipo adzapukusa mutu wake.+
16 Choncho dziko lawo lidzakhala chinthu chochititsa mantha+Komanso chimene anthu azidzachiimbira mluzu mpaka kalekale.+ Aliyense wodutsa pafupi ndi dzikoli adzaliyangʼanitsitsa mwamantha ndipo adzapukusa mutu wake.+