Yeremiya 18:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kodi akuyenera kubwezera zinthu zoipa pa zinthu zabwino? Iwo akumba dzenje kuti achotse moyo wanga.+ Kumbukirani kuti ndinkaima pamaso panu nʼkumalankhula zabwino zokhudza anthu amenewa,Kuti muwachotsere mkwiyo wanu.
20 Kodi akuyenera kubwezera zinthu zoipa pa zinthu zabwino? Iwo akumba dzenje kuti achotse moyo wanga.+ Kumbukirani kuti ndinkaima pamaso panu nʼkumalankhula zabwino zokhudza anthu amenewa,Kuti muwachotsere mkwiyo wanu.