Yeremiya 18:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Choncho lolani kuti ana awo afe ndi njala,Komanso aphedwe ndi lupanga.+ Akazi awo akhale amasiye ndipo ana a akaziwo afe.+ Amuna awo afe ndi mliri woopsaNdipo anyamata awo aphedwe ndi lupanga pankhondo.+
21 Choncho lolani kuti ana awo afe ndi njala,Komanso aphedwe ndi lupanga.+ Akazi awo akhale amasiye ndipo ana a akaziwo afe.+ Amuna awo afe ndi mliri woopsaNdipo anyamata awo aphedwe ndi lupanga pankhondo.+