-
Yeremiya 19:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Ukawauze kuti, ‘Tamverani mawu a Yehova inu mafumu a Yuda ndi inu anthu amene mukukhala mu Yerusalemu. Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti:
‘“Ine ndatsala pangʼono kubweretsa tsoka pamalo ano ndipo aliyense akadzamva za tsoka limeneli, mʼmakutu mwake mudzachita phokoso.
-