Yeremiya 19:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho taonani! masiku akubwera,” akutero Yehova, “pamene sadzatchulanso malowo kuti Tofeti kapena Chigwa cha Mwana wa Hinomu, koma adzawatchula kuti Chigwa Chopherako Anthu.+
6 Choncho taonani! masiku akubwera,” akutero Yehova, “pamene sadzatchulanso malowo kuti Tofeti kapena Chigwa cha Mwana wa Hinomu, koma adzawatchula kuti Chigwa Chopherako Anthu.+