-
Yeremiya 19:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 ‘Izi ndi zimene ndidzachite ndi malo awa ndiponso ndi anthu onse amene akukhala mmenemu kuti mzindawu ukhale ngati Tofeti,’ akutero Yehova.
-