Yeremiya 19:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti, ‘Ine ndikubweretsera mzinda uwu ndi matauni ake onse masoka onse amene ndinanena, chifukwa anthu ake aumitsa mitima yawo nʼkukana* kumvera mawu anga.’”+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:15 Yeremiya, tsa. 159
15 “Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti, ‘Ine ndikubweretsera mzinda uwu ndi matauni ake onse masoka onse amene ndinanena, chifukwa anthu ake aumitsa mitima yawo nʼkukana* kumvera mawu anga.’”+