Yeremiya 20:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno pa tsiku lotsatira, Pasuri atamasula Yeremiya mʼmatangadzawo, Yeremiya anamuuza kuti: “Yehova wanena kuti dzina lako silikhalanso Pasuri koma Chochititsa Mantha Paliponse.+
3 Ndiyeno pa tsiku lotsatira, Pasuri atamasula Yeremiya mʼmatangadzawo, Yeremiya anamuuza kuti: “Yehova wanena kuti dzina lako silikhalanso Pasuri koma Chochititsa Mantha Paliponse.+