Yeremiya 20:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndipo chuma chonse chamumzindawu, katundu wawo yense, zinthu zawo zonse zamtengo wapatali ndi chuma chonse cha mafumu a Yuda ndidzazipereka mʼmanja mwa adani awo.+ Adaniwo adzatenga zinthu zimenezi nʼkupita nazo ku Babulo.+
5 Ndipo chuma chonse chamumzindawu, katundu wawo yense, zinthu zawo zonse zamtengo wapatali ndi chuma chonse cha mafumu a Yuda ndidzazipereka mʼmanja mwa adani awo.+ Adaniwo adzatenga zinthu zimenezi nʼkupita nazo ku Babulo.+