Yeremiya 20:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma iwe Pasuri ndi anthu onse amene amakhala mʼnyumba yako, mudzapita ku ukapolo. Iweyo udzapita ku Babulo ndipo udzafera kumeneko nʼkuikidwa mʼmanda komweko limodzi ndi anzako onse, chifukwa walosera zabodza kwa iwo.’”+
6 Koma iwe Pasuri ndi anthu onse amene amakhala mʼnyumba yako, mudzapita ku ukapolo. Iweyo udzapita ku Babulo ndipo udzafera kumeneko nʼkuikidwa mʼmanda komweko limodzi ndi anzako onse, chifukwa walosera zabodza kwa iwo.’”+