Yeremiya 20:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mwandipusitsa* inu Yehova, ndithu mwandipusitsa. Mwagwiritsa ntchito mphamvu zanu pa ine ndipo mwapambana.+ Ndakhala chinthu choseketsa tsiku lonse.Aliyense akungondinyoza.+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 20:7 Yeremiya, ptsa. 36-37 Nsanja ya Olonda,3/15/2007, tsa. 95/1/1989, tsa. 31
7 Mwandipusitsa* inu Yehova, ndithu mwandipusitsa. Mwagwiritsa ntchito mphamvu zanu pa ine ndipo mwapambana.+ Ndakhala chinthu choseketsa tsiku lonse.Aliyense akungondinyoza.+