Yeremiya 20:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Nthawi zonse ndikafuna kulankhula, ndimafuula kuti,“Chiwawa ndi chiwonongeko!” Kwa ine mawu a Yehova achititsa kuti ndizinyozedwa ndi kusekedwa tsiku lonse.+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 20:8 Yeremiya, tsa. 118
8 Nthawi zonse ndikafuna kulankhula, ndimafuula kuti,“Chiwawa ndi chiwonongeko!” Kwa ine mawu a Yehova achititsa kuti ndizinyozedwa ndi kusekedwa tsiku lonse.+