Yeremiya 20:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma inu Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, mumafufuza munthu wolungama.Mumaona maganizo a munthu* komanso mtima wake.+ Ndiloleni ndione mukuwapatsa chilango,+Chifukwa mlandu wanga ndausiya mʼmanja mwanu.+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 20:12 Yeremiya, ptsa. 147-149
12 Koma inu Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, mumafufuza munthu wolungama.Mumaona maganizo a munthu* komanso mtima wake.+ Ndiloleni ndione mukuwapatsa chilango,+Chifukwa mlandu wanga ndausiya mʼmanja mwanu.+