-
Yeremiya 20:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Atembereredwe munthu amene anabweretsa uthenga wabwino kwa bambo anga powauza kuti:
“Mkazi wako wakuberekera mwana wamwamuna, kamnyamata!”
Nʼkuchititsa kuti bambo anga asangalale kwambiri.
-