Yeremiya 21:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Yeremiya analandira mawu ochokera kwa Yehova pamene Mfumu Zedekiya+ inatumiza Pasuri+ mwana wa Malikiya ndi Zefaniya+ mwana wa Maaseya, wansembe, kuti akamupemphe kuti:
21 Yeremiya analandira mawu ochokera kwa Yehova pamene Mfumu Zedekiya+ inatumiza Pasuri+ mwana wa Malikiya ndi Zefaniya+ mwana wa Maaseya, wansembe, kuti akamupemphe kuti: