Yeremiya 21:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Chonde tifunsire kwa Yehova chifukwa Nebukadinezara,* mfumu ya ku Babulo, akufuna kuchita nafe nkhondo.+ Mwina Yehova atichitira imodzi mwa ntchito zake zodabwitsa moti Nebukadinezarayo atichokera.”+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:2 Yeremiya, ptsa. 55-56
2 “Chonde tifunsire kwa Yehova chifukwa Nebukadinezara,* mfumu ya ku Babulo, akufuna kuchita nafe nkhondo.+ Mwina Yehova atichitira imodzi mwa ntchito zake zodabwitsa moti Nebukadinezarayo atichokera.”+