-
Yeremiya 21:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 ‘Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti: “Ine ndichititsa zida zankhondo zimene zili mʼmanja mwanu kukutembenukirani. Zimenezi ndi zida zimene mukugwiritsa ntchito pomenyana ndi mfumu ya Babulo+ ndi Akasidi amene akuzungulirani kunja kwa mpanda wanu. Ndipo ine ndidzasonkhanitsa zidazo pakati pa mzindawu.
-