Yeremiya 21:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 ‘“Ndatsimikiza kubweretsa tsoka pamzinda uwu, osati zinthu zabwino,”*+ akutero Yehova. “Mzindawu udzaperekedwa mʼmanja mwa mfumu ya Babulo+ ndipo adzauwotcha ndi moto.”+
10 ‘“Ndatsimikiza kubweretsa tsoka pamzinda uwu, osati zinthu zabwino,”*+ akutero Yehova. “Mzindawu udzaperekedwa mʼmanja mwa mfumu ya Babulo+ ndipo adzauwotcha ndi moto.”+