-
Yeremiya 22:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Ukanene kuti, ‘Tamverani mawu a Yehova, inu mfumu ya Yuda amene mwakhala pampando wachifumu wa Davide. Mumve mawu amenewa inuyo, atumiki anu komanso anthu anu amene amalowa pamageti awa.
-