Yeremiya 22:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mukamvera mawu amenewa mosamala, mafumu amene amakhala pampando wachifumu wa Davide+ adzalowa pamageti a nyumba iyi. Iwowo, atumiki awo komanso anthu awo adzalowa pamageti amenewa atakwera magaleta ndi mahatchi.”’+
4 Mukamvera mawu amenewa mosamala, mafumu amene amakhala pampando wachifumu wa Davide+ adzalowa pamageti a nyumba iyi. Iwowo, atumiki awo komanso anthu awo adzalowa pamageti amenewa atakwera magaleta ndi mahatchi.”’+