Yeremiya 22:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ponena za nyumba ya mfumu ya Yuda, Yehova wanena kuti,‘Kwa ine, iwe uli ngati Giliyadi,Uli ngati nsonga ya phiri la ku Lebanoni. Koma ndidzakusandutsa chipululu,Ndipo mʼmizinda yako yonse simudzapezeka aliyense wokhalamo.+
6 Ponena za nyumba ya mfumu ya Yuda, Yehova wanena kuti,‘Kwa ine, iwe uli ngati Giliyadi,Uli ngati nsonga ya phiri la ku Lebanoni. Koma ndidzakusandutsa chipululu,Ndipo mʼmizinda yako yonse simudzapezeka aliyense wokhalamo.+