Yeremiya 22:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anthu ochokera mʼmitundu yambiri adzadutsa pafupi ndi mzindawu ndipo adzafunsana kuti: “Nʼchifukwa chiyani Yehova anachitira mzinda waukuluwu zinthu zimenezi?”+
8 Anthu ochokera mʼmitundu yambiri adzadutsa pafupi ndi mzindawu ndipo adzafunsana kuti: “Nʼchifukwa chiyani Yehova anachitira mzinda waukuluwu zinthu zimenezi?”+