Yeremiya 22:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndipo adzayankha kuti: “Chifukwa chakuti anthu amumzindawu anasiya pangano la Yehova Mulungu wawo nʼkuyamba kulambira milungu ina ndiponso kuitumikira.”’+
9 Ndipo adzayankha kuti: “Chifukwa chakuti anthu amumzindawu anasiya pangano la Yehova Mulungu wawo nʼkuyamba kulambira milungu ina ndiponso kuitumikira.”’+