Yeremiya 22:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ponena za Salumu*+ mwana wa Yosiya, mfumu ya Yuda, amene akulamulira mʼmalo mwa bambo ake Yosiya,+ amene anachoka mʼdziko lino kupita ku ukapolo, Yehova wanena kuti: ‘Sadzabwereranso kwawo. Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:11 Yeremiya, ptsa. 158-159
11 Ponena za Salumu*+ mwana wa Yosiya, mfumu ya Yuda, amene akulamulira mʼmalo mwa bambo ake Yosiya,+ amene anachoka mʼdziko lino kupita ku ukapolo, Yehova wanena kuti: ‘Sadzabwereranso kwawo.