Yeremiya 22:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsoka kwa munthu amene amamanga nyumba yakeKomanso zipinda zake zamʼmwamba mopanda chilungamo.Amene amagwiritsa anthu ntchito kwaulere,Ndipo amakana kuwapatsa malipiro awo.+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:13 Yeremiya, tsa. 140
13 Tsoka kwa munthu amene amamanga nyumba yakeKomanso zipinda zake zamʼmwamba mopanda chilungamo.Amene amagwiritsa anthu ntchito kwaulere,Ndipo amakana kuwapatsa malipiro awo.+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:13 Yeremiya, tsa. 140