-
Yeremiya 22:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Amene amanena kuti, ‘Ndimanga nyumba yaikulu
Yokhala ndi zipinda zikuluzikulu zamʼmwamba.
Ndidzaiikira mawindo
Nʼkuyala matabwa a mkungudza mʼmakoma ake ndipo ndidzaipaka penti wofiira.’
-