Yeremiya 22:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kodi ukuganiza kuti upitiriza kulamulira chifukwa chakuti ukugwiritsa ntchito kwambiri matabwa a mkungudzawa kuposa anthu ena? Bambo akonso ankadya komanso kumwaKoma ankachita zinthu motsatira malamulo komanso mwachilungamo,+Ndipo zinthu zinawayendera bwino. Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:15 Yeremiya, ptsa. 140-141
15 Kodi ukuganiza kuti upitiriza kulamulira chifukwa chakuti ukugwiritsa ntchito kwambiri matabwa a mkungudzawa kuposa anthu ena? Bambo akonso ankadya komanso kumwaKoma ankachita zinthu motsatira malamulo komanso mwachilungamo,+Ndipo zinthu zinawayendera bwino.