-
Yeremiya 22:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 ‘Koma maso ako ndi mtima wako zili pa kupeza phindu mwachinyengo,
Kukhetsa magazi a anthu osalakwa,
Komanso kuba mwachinyengo ndi kulanda anthu zinthu zawo basi.’
-