Yeremiya 22:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndinalankhula nawe pamene unkaona kuti ndiwe wotetezeka. Koma iwe unanena kuti, ‘Sindimvera.’+ Wakhala ukuchita zimenezi kuyambira uli wachinyamata,Chifukwa wakhala usakumvera mawu anga.+
21 Ndinalankhula nawe pamene unkaona kuti ndiwe wotetezeka. Koma iwe unanena kuti, ‘Sindimvera.’+ Wakhala ukuchita zimenezi kuyambira uli wachinyamata,Chifukwa wakhala usakumvera mawu anga.+