Yeremiya 22:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mphepo idzaweta abusa ako onse+Ndipo anthu amene akukukonda kwambiri adzatengedwa kupita ku ukapolo. Pa nthawi imeneyo udzachititsidwa manyazi ndipo udzanyozeka chifukwa cha masoka onse amene adzakugwere.
22 Mphepo idzaweta abusa ako onse+Ndipo anthu amene akukukonda kwambiri adzatengedwa kupita ku ukapolo. Pa nthawi imeneyo udzachititsidwa manyazi ndipo udzanyozeka chifukwa cha masoka onse amene adzakugwere.