Yeremiya 22:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 ‘Pali ine, Mulungu wamoyo,’ akutero Yehova, ‘ngakhale iwe Koniya*+ mwana wa Yehoyakimu,+ mfumu ya Yuda, utakhala mphete yodindira kudzanja langa lamanja, ndingakuvule!
24 ‘Pali ine, Mulungu wamoyo,’ akutero Yehova, ‘ngakhale iwe Koniya*+ mwana wa Yehoyakimu,+ mfumu ya Yuda, utakhala mphete yodindira kudzanja langa lamanja, ndingakuvule!