Yeremiya 22:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndidzakupereka mʼmanja mwa anthu amene akufuna kuchotsa moyo wako, mʼmanja mwa anthu amene umawaopa, mʼmanja mwa Mfumu Nebukadinezara* ya ku Babulo ndiponso mʼmanja mwa Akasidi.+
25 Ndidzakupereka mʼmanja mwa anthu amene akufuna kuchotsa moyo wako, mʼmanja mwa anthu amene umawaopa, mʼmanja mwa Mfumu Nebukadinezara* ya ku Babulo ndiponso mʼmanja mwa Akasidi.+