Yeremiya 22:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Kodi munthu uyu Koniya, wangokhala chiwiya chonyozeka komanso chophwanyika,Chiwiya chimene palibe amene akuchifuna? Nʼchifukwa chiyani iyeyu ndi ana ake agwetsedwa pansiNʼkuponyedwa mʼdziko limene sakulidziwa?’+
28 Kodi munthu uyu Koniya, wangokhala chiwiya chonyozeka komanso chophwanyika,Chiwiya chimene palibe amene akuchifuna? Nʼchifukwa chiyani iyeyu ndi ana ake agwetsedwa pansiNʼkuponyedwa mʼdziko limene sakulidziwa?’+