Yeremiya 22:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Yehova wanena kuti: ‘Lembani kuti munthu uyu alibe ana,Munthu amene zinthu sizidzamuyendera bwino pa moyo wake.*Chifukwa palibe mwana wake aliyense, amene adzakwanitseKukhala pampando wachifumu wa Davide nʼkuyambiranso kulamulira mu Yuda.’”+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:30 Nsanja ya Olonda,3/15/2007, tsa. 10
30 Yehova wanena kuti: ‘Lembani kuti munthu uyu alibe ana,Munthu amene zinthu sizidzamuyendera bwino pa moyo wake.*Chifukwa palibe mwana wake aliyense, amene adzakwanitseKukhala pampando wachifumu wa Davide nʼkuyambiranso kulamulira mu Yuda.’”+