Yeremiya 23:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Choncho Yehova Mulungu wa Isiraeli wadzudzula abusa amene akuweta anthu ake kuti: “Inu mwabalalitsa nkhosa zanga. Munapitiriza kuzimwaza ndipo simunazisamalire.”+ “Tsopano ndikulangani chifukwa cha zochita zanu zoipa,” akutero Yehova.
2 Choncho Yehova Mulungu wa Isiraeli wadzudzula abusa amene akuweta anthu ake kuti: “Inu mwabalalitsa nkhosa zanga. Munapitiriza kuzimwaza ndipo simunazisamalire.”+ “Tsopano ndikulangani chifukwa cha zochita zanu zoipa,” akutero Yehova.