Yeremiya 23:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma adzalumbira kuti, ‘Pali Yehova Mulungu wamoyo amene anatulutsa a mʼnyumba ya Isiraeli nʼkuwabweretsa kuno kuchokera mʼdziko lakumpoto komanso kuchokera mʼmayiko onse kumene ndinawabalalitsiraʼ ndipo adzakhala mʼdziko lawo.”+
8 Koma adzalumbira kuti, ‘Pali Yehova Mulungu wamoyo amene anatulutsa a mʼnyumba ya Isiraeli nʼkuwabweretsa kuno kuchokera mʼdziko lakumpoto komanso kuchokera mʼmayiko onse kumene ndinawabalalitsiraʼ ndipo adzakhala mʼdziko lawo.”+