-
Yeremiya 23:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Ponena za aneneriwo ndikuti:
Mtima wanga wasweka mkati mwanga.
Mafupa anga onse akunjenjemera.
Ndili ngati munthu woledzera
Komanso ngati munthu amene wagonjetsedwa ndi vinyo,
Chifukwa cha Yehova komanso chifukwa cha mawu ake oyera.
-