Yeremiya 25:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Awa ndi mawu amene Yeremiya anauzidwa onena za anthu onse a mu Yuda mʼchaka cha 4 cha ulamuliro wa Yehoyakimu+ mwana wa Yosiya, mfumu ya Yuda, chimenenso chinali chaka choyamba cha ulamuliro wa Nebukadinezara* mfumu ya Babulo. Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 25:1 Ulosi wa Danieli, ptsa. 18-19
25 Awa ndi mawu amene Yeremiya anauzidwa onena za anthu onse a mu Yuda mʼchaka cha 4 cha ulamuliro wa Yehoyakimu+ mwana wa Yosiya, mfumu ya Yuda, chimenenso chinali chaka choyamba cha ulamuliro wa Nebukadinezara* mfumu ya Babulo.