Yeremiya 25:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Kuyambira mʼchaka cha 13 cha ulamuliro wa Yosiya+ mwana wa Amoni, mfumu ya Yuda, mpaka lero, zaka 23 zonsezi, Yehova wakhala akundiuza mawu ndipo ine ndakhala ndikukuuzani mawuwo mobwerezabwereza,* koma inu simunamvere.+
3 “Kuyambira mʼchaka cha 13 cha ulamuliro wa Yosiya+ mwana wa Amoni, mfumu ya Yuda, mpaka lero, zaka 23 zonsezi, Yehova wakhala akundiuza mawu ndipo ine ndakhala ndikukuuzani mawuwo mobwerezabwereza,* koma inu simunamvere.+