Yeremiya 25:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Yehova anakutumizirani atumiki ake onse omwe anali aneneri. Ankawatumiza mobwerezabwereza* koma inu simunawamvere kapena kutchera khutu lanu kuti mumvetsere.+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 25:4 Nsanja ya Olonda,4/1/1988, tsa. 22
4 Yehova anakutumizirani atumiki ake onse omwe anali aneneri. Ankawatumiza mobwerezabwereza* koma inu simunawamvere kapena kutchera khutu lanu kuti mumvetsere.+