Yeremiya 25:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iwo ankakuuzani kuti, ‘Chonde, aliyense wa inu atembenuke nʼkusiya njira zake zoipa ndi zochita zake zoipa.+ Mukatero mudzapitiriza kukhala kwa nthawi yaitali mʼdziko limene Yehova anakupatsani kalekale, inuyo ndi makolo anu. Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 25:5 Nsanja ya Olonda,3/1/1994, tsa. 19
5 Iwo ankakuuzani kuti, ‘Chonde, aliyense wa inu atembenuke nʼkusiya njira zake zoipa ndi zochita zake zoipa.+ Mukatero mudzapitiriza kukhala kwa nthawi yaitali mʼdziko limene Yehova anakupatsani kalekale, inuyo ndi makolo anu.