Yeremiya 25:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 ‘Koma simunandimvere,’ akutero Yehova, ‘Mʼmalomwake munandikhumudwitsa ndi ntchito ya manja anu, zimene zinachititsa kuti tsoka likugwereni.’+
7 ‘Koma simunandimvere,’ akutero Yehova, ‘Mʼmalomwake munandikhumudwitsa ndi ntchito ya manja anu, zimene zinachititsa kuti tsoka likugwereni.’+