Yeremiya 25:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndidzathetsa phokoso lachikondwerero ndi phokoso lakusangalala mʼmalowo.+ Ndidzathetsanso mawu osangalala a mkwati ndi a mkwatibwi.+ Simudzamvekanso kupera kwa mphero ndipo simudzaonekanso kuwala kwa nyale. Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 25:10 Nsanja ya Olonda,7/1/2015, tsa. 156/1/2014, tsa. 93/1/1994, ptsa. 19-20 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 270
10 Ndidzathetsa phokoso lachikondwerero ndi phokoso lakusangalala mʼmalowo.+ Ndidzathetsanso mawu osangalala a mkwati ndi a mkwatibwi.+ Simudzamvekanso kupera kwa mphero ndipo simudzaonekanso kuwala kwa nyale.
25:10 Nsanja ya Olonda,7/1/2015, tsa. 156/1/2014, tsa. 93/1/1994, ptsa. 19-20 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 270