Yeremiya 25:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 ‘Ndiyeno zaka 70 zimenezo zikadzakwana,+ ndidzalanga mfumu ya Babulo ndi mtundu umenewo chifukwa cha zolakwa zawo.+ Ndipo dziko la Akasidi ndidzalisandutsa bwinja mpaka kalekale,’ akutero Yehova.+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 25:12 Nsanja ya Olonda,3/1/1994, tsa. 20
12 ‘Ndiyeno zaka 70 zimenezo zikadzakwana,+ ndidzalanga mfumu ya Babulo ndi mtundu umenewo chifukwa cha zolakwa zawo.+ Ndipo dziko la Akasidi ndidzalisandutsa bwinja mpaka kalekale,’ akutero Yehova.+