Yeremiya 25:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Chifukwa mitundu yambiri ndi mafumu otchuka+ adzawagwiritsa ntchito ngati akapolo+ ndipo ndidzawabwezera mogwirizana ndi zochita zawo komanso ntchito ya manja awo.’”+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 25:14 Nsanja ya Olonda,3/1/1994, tsa. 20
14 Chifukwa mitundu yambiri ndi mafumu otchuka+ adzawagwiritsa ntchito ngati akapolo+ ndipo ndidzawabwezera mogwirizana ndi zochita zawo komanso ntchito ya manja awo.’”+