Yeremiya 25:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho ndinatenga kapu imene inali mʼdzanja la Yehova ndipo ndinamwetsa mitundu yonse imene Yehova ananditumizako. Mitunduyo ndi iyi:+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 25:17 Nsanja ya Olonda,3/1/1994, ptsa. 20-21
17 Choncho ndinatenga kapu imene inali mʼdzanja la Yehova ndipo ndinamwetsa mitundu yonse imene Yehova ananditumizako. Mitunduyo ndi iyi:+