Yeremiya 25:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 mafumu onse a Turo, mafumu onse a Sidoni+ ndi mafumu a pachilumba chamʼnyanja.