Yeremiya 25:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 “Ndiyeno ukawauze kuti, ‘Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Mulungu wa Isiraeli wanena kuti: “Imwani ndipo muledzere, musanze ndi kugwa osadzukanso+ chifukwa cha lupanga limene ndikutumiza pakati panu.”’ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 25:27 Nsanja ya Olonda,3/1/1994, tsa. 21
27 “Ndiyeno ukawauze kuti, ‘Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Mulungu wa Isiraeli wanena kuti: “Imwani ndipo muledzere, musanze ndi kugwa osadzukanso+ chifukwa cha lupanga limene ndikutumiza pakati panu.”’